Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndi zimene munthu akuyenera kuchita.+

  • Yeremiya 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga, ndipo ndidzakhala Mulungu wanu, inuyo mudzakhala anthu anga.+ Muziyenda mʼnjira imene ndakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+

  • Aroma 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mdulidwe+ ndi waphindu pokhapokha ngati iweyo umatsatiradi Chilamulo.+ Koma ngati umaphwanya Chilamulo, mdulidwe wako ndi wopanda ntchito.

  • Agalatiya 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chifukwa ngati munthu ali wogwirizana ndi Khristu Yesu, kudulidwa kapena kusadulidwa kumakhala kopanda ntchito.+ Koma chofunika kwambiri nʼkukhala ndi chikhulupiriro chimene chimaonekera posonyeza chikondi.

  • 1 Yohane 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kukonda Mulungu kumatanthauza kutsatira malamulo ake,+ ndipo malamulo akewo si ovuta kuwatsatira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena