Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 28:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Wosangalala ndi munthu amene nthawi zonse amasamala zochita zake,*

      Koma amene amaumitsa mtima wake adzakumana ndi tsoka.+

  • Luka 22:33, 34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Kenako iye anauza Yesu kuti: “Ambuye, ndine wokonzeka kupita nanu limodzi kundende kapena kufa nanu limodzi.”+ 34 Koma iye anati: “Ndikukuuza iwe Petulo, tambala asanalire lero, undikana katatu kuti sukundidziwa.”+

  • Agalatiya 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Abale, ngati munthu wapatuka nʼkuyamba kulowera njira yolakwika mosazindikira, inu amene ndi oyenerera mwauzimu, yesani kuthandiza munthu woteroyo ndi mzimu wofatsa.+ Koma pamene mukuchita zimenezi musamale,+ kuopera kuti inunso mungayesedwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena