Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+ Afilipi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu,* anadzichepetsa ndipo anakhala womvera mpaka imfa,+ inde imfa yapamtengo wozunzikirapo.*+
39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+
8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu,* anadzichepetsa ndipo anakhala womvera mpaka imfa,+ inde imfa yapamtengo wozunzikirapo.*+