-
Mateyu 10:2-4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mayina a atumwi 12 ndi awa:+ Simoni, amene ankatchulidwa kuti Petulo*+ ndi Andireya+ mchimwene wake. Yakobo mwana wa Zebedayo ndi mchimwene wake Yohane.+ 3 Filipo ndi Batolomeyo,+ Tomasi+ ndi Mateyu+ wokhometsa msonkho, Yakobo mwana wa Alifeyo ndi Tadeyo. 4 Simoni Kananiya* ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anapereka Yesu.+
-
-
Luka 6:13-16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kutacha, anaitana ophunzira ake nʼkusankhapo 12, amenenso anawapatsa dzina lakuti atumwi.+ 14 Iye anasankha Simoni, amene ankatchulidwa kuti Petulo, ndi Andireya mchimwene wake. Anasankhanso Yakobo, Yohane, Filipo,+ Batolomeyo, 15 Mateyu, Tomasi,+ Yakobo mwana wa Alifeyo, ndi Simoni wotchedwa “wakhama.” 16 Komanso anasankha Yudasi mwana wa Yakobo ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anamupereka.
-