MASALIMO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Yehova ndi Woweruza wolungama
“Ndiweruzeni inu Yehova” (8)
-
Yehova amanyamuka nʼkuchitapo kanthu
Mawu a Mulungu ndi oyera (6)
-
Kupulumutsidwa kwa mfumu yodzozedwa ya Mulungu
Ena amadalira magaleta ndi mahatchi, “koma ife timadalira dzina la Yehova” (7)
-
Mfumu yaulemerero yalowa mʼmageti
‘Dziko lapansi ndi la Yehova’ (1)
-
Mulungu anayankha pemphero la amene analemba salimo
‘Yehova ndi mphamvu yanga komanso chishango changa’ (7)
-
Kulira kunasanduka chisangalalo
Mulungu amakomera mtima anthu kwa moyo wawo wonse (5)
-
Anthu amene amadalira Yehova zinthu zimawayendera bwino
-
Pemphero lopempha kuthandizidwa pa nthawi youkiridwa ndi adani
“Mulungu ndi amene amandithandiza” (4)
-
Pali Mulungu amene amaweruza dziko lapansi
Pemphero lopempha kuti anthu oipa alangidwe (6-8)
-
Mulungu ndi nsanja yolimba imene imateteza kwa adani
“Ndidzakhala mlendo mutenti yanu” (4)
-
Nditetezeni ku ziwembu zobisika
“Mulungu adzawalasa” (7)
-
Anapempha kuti amuthandize mwamsanga
“Ndithandizeni mwamsanga” (5)
-
Ulamuliro wamtendere wa mfumu ya Mulungu
-
Mulungu amaweruza mwachilungamo
Anthu oipa adzamwa zamʼkapu ya Yehova (8)
-
Mulungu ankasamalira Aisiraeli koma iwo analibe chikhulupiriro
-
Ziyoni ndi mzinda wa Mulungu woona
Amene anabadwira mu Ziyoni (4-6)
-
Imbani za chikondi chokhulupirika cha Yehova
-
Yehova ndi Mpulumutsi komanso Woweruza wolungama
Chipulumutso cha Yehova chadziwika (2, 3)
-
Zimene Yehova anachitira anthu ake posonyeza kuti ndi wokhulupirika
-
Anthu a mitundu yonse akupemphedwa kuti atamande Yehova
Chikondi chokhulupirika cha Mulungu nʼchachikulu (2)
-
Kuyamikira mawu amtengo wapatali a Mulungu
“Kodi wachinyamata angakhale bwanji woyera pa moyo wake?” (9)
“Ndimakonda kwambiri zikumbutso zanu” (24)
“Ndimakonda kwambiri chilamulo chanu!” (97)
“Wozindikira kwambiri kuposa aphunzitsi anga onse” (99)
“Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga” (105)
“Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha” (160)
Amene amakonda chilamulo cha Mulungu amakhala ndi mtendere (165)
-
Kuukiridwa koma osagonjetsedwa
Odana ndi Ziyoni achititsidwa manyazi (5)
-
Wokhutira ngati mwana amene anamusiyitsa kuyamwa
“Sindilakalaka zinthu zapamwamba kwambiri” (1)
-
Kutamanda Mulungu usiku
“Muzikhala oyera mukamapemphera mutakweza manja anu” (2)