Salimo
Nyimbo Yokwerera Kumzinda.
129 “Akhala akundiukira nthawi zonse kuyambira ndili mnyamata,”+
Tsopano Isiraeli anene kuti,
2 “Akhala akundiukira nthawi zonse kuyambira ndili mnyamata,+
Koma sanandigonjetse.+
6 Adzakhala ngati udzu umene wamera padenga
Umene umauma usanazulidwe,
7 Umene sungadzaze mʼdzanja la munthu amene akukolola
Kapena mʼmanja mwa munthu amene akumanga mitolo ya zokolola.
8 Anthu odutsa sadzanena kuti:
“Madalitso a Yehova akhale nanu.
Tikukudalitsani mʼdzina la Yehova.”