Zamkatimu
January 15, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA
FEBRUARY 27, 2012–MARCH 4, 2012
Akhristu Oona Amalemekeza Mawu a Mulungu
TSAMBA 4 • NYIMBO: 113, 116
MARCH 5-11, 2012
Phunzirani Kukhala Maso Kuchokera kwa Atumwi a Yesu
TSAMBA 9 • NYIMBO: 125, 43
MARCH 12-18, 2012
Phunzirani Kuchokera ku Choonadi cha M’chilamulo
TSAMBA 16 • NYIMBO: 107, 13
MARCH 19-25, 2012
Tizipereka Nsembe kwa Yehova ndi Moyo Wathu Wonse
TSAMBA 21 • NYIMBO: 66, 56
MARCH 26, 2012–APRIL 1, 2012
Ansembe Achifumu Amene Adzapindulitse Anthu Onse
TSAMBA 26 • NYIMBO: 60, 102
CHOLINGA CHA NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI YOPHUNZIRA 1 TSAMBA 4-8
Nkhaniyi ikusonyeza kuti kuyambira kalekale Akhristu oona akhala akuyesetsa kuti azitsogoleredwa ndi Mawu a Mulungu. Tionanso m’nkhaniyi lemba lathu la chaka cha 2012.
NKHANI YOPHUNZIRA 2 TSAMBA 9-13
Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zitatu zimene tingaphunzire kuchokera kwa atumwi ndiponso Akhristu ena oyambirira pa nkhani ya kukhala maso. Itithandiza kukhala ofunitsitsa kuchitira umboni mokwanira za Ufumu wa Mulungu.
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 TSAMBA 16-25
Chilamulo cha Mose chinkalamula kuti Aisiraeli azipereka nsembe kwa Yehova pa nthawi zosiyanasiyana. Akhristu sayenera kutsatira Chilamulochi. Koma angaphunzire zambiri m’Chilamulochi pa nkhani ya mtima woyamikira womwe Yehova amafuna kuti anthu ake azikhala nawo pomulambira. Nkhanizi zikufotokoza zimenezi.
NKHANI YOPHUNZIRA 5 TSAMBA 26-30
Zimene anthu akufunika kwambiri ndi kugwirizanitsidwa ndi Mulungu. Nkhaniyi ikufotokoza mmene ansembe achifumu adzathandizire kuti zimenezi zitheke. Ikufotokozanso madalitso amene ifeyo tidzapeza.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Zimene Zasintha M’magazini Yophunzira
14 ‘Kodi Mmene Ndililimu Ndingakwanitse Kulalikira?’
15 Zomwe Mungachite Kuti Muzipindula Ndiponso Kusangalala Mukamaphunzira Baibulo
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Banja limene likuchita upainiya ndiponso limene laphunzira chinenero cha Tzotzil likulalikira kwa banja lolankhula chinenerocho. Ali kumsika wa mumzinda wa San Cristóbal de las Casas, ku Mexico.
MEXICO
KULI ANTHU OKWANA
108,782,804
KULI OFALITSA OKWANA
710,454
ZINENERO ZIMENE AMAZIMASULIRA
Zinenero 30 za kumeneko