Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2014
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Ankagwiritsa Ntchito Baibulo Poyankha Funso Lililonse (I. Lamela), 4/1
Ndinkamenya Nkhondo Yolimbana ndi Kupanda Chilungamo Komanso Chiwawa (A. Touma), 8/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
Kodi oukitsidwa padzikoli sadzakwatira kapena kukwatiwa? (Luka 20:34-36), 8/15
Kodi Yehova sadzalola kuti Mkhristu avutike ndi njala? (Sal. 37:25; Mat. 6:33), 9/15
MBIRI YA MOYO WANGA
Kutumikira Mulungu Kwandithandiza Kuti Ndikhale Wosangalala (P. Carrbello), 9/1
Mavuto Andithandiza Kulimbitsa Ubwenzi ndi Yehova (M. Morlans), 3/1
MBONI ZA YEHOVA
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
NKHANI ZOPHUNZIRA
Kodi Ufumu Umene Walamulira Zaka 100 Umakukhudzani Bwanji? 1/15
Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu Chifukwa Ndi Amoyo, 8/15
N’chiyani Chimakutsimikizirani Kuti Muli M’gulu la Yehova? 9/15
Tumikirani Mulungu Mokhulupirika Pokumana ndi “Masautso Ambiri,” 9/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Kodi Apitiriza Kuwononga Dzikoli N’kufika Poti Silingakonzedwenso? 9/1
Kodi Malamulo Amene Mulungu Anapatsa Aisiraeli Anali Achilungamo? 9/1
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera Kuti Ufumu Ubwere? 10/1
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera, Tizipemphera Bwanji? 7/1
N’chifukwa Chiyani Zigawenga Ankazithyola Miyendo Akamazipha? 5/1
Nkhondo Yomwe Inasintha Dziko Lonse (Nkhondo Yoyamba ya Padziko Lonse), 2/1