Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 May tsamba 8
  • Kusamalira Malo Athu Olambirira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kusamalira Malo Athu Olambirira
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Zomwe Tonse Tingachite Posamalira Malo Athu Olambirira
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Tizilemekeza Malo Athu Olambirira Yehova
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Malo Olambirira Yehova
    Gulu Lochita Chifuniro cha Mulungu
  • Mmene Anthu Akuwonjezekera Pakufunika Nyumba Zina Mwamsanga
    Nsanja ya Olonda—2002
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 May tsamba 8

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kusamalira Malo Athu Olambirira

Njira zimene tingathandizire kusamalira Nyumba ya Ufumu: kupenta, kuika kalapeti, kukonza magetsi, komanso kupereka ndalama

Nyumba zathu za Ufumu si nyumba wamba, koma ndi malo amene timalambirirako Yehova. Ndiye kodi aliyense angatani kuti azigwira nawo ntchito yosamalira Nyumba ya Ufumu? Onerani vidiyo yakuti Kusamalira Malo Athu Olambirira, ndipo kenako kambiranani mafunso otsatirawa:

  1. Kodi m’Nyumba ya Ufumu mumachitika zotani?

  2. N’chifukwa chiyani tiyenera kuyesetsa kukonza Nyumba ya Ufumu kuti izikhala yaukhondo komanso yooneka bwino?

  3. Kodi ndi ndani amene ayenera kukonza Nyumba ya Ufumu?

  4. Kodi kupewa ngozi n’kofunika bwanji, nanga m’vidiyoyi taona zitsanzo ziti zimene zingatithandize kupewa ngozi?

  5. Kodi tingalemekeze bwanji Yehova ndi ndalama zimene timapereka?

KODI INEYO NDINGATHANDIZE NAWO BWANJI?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena