May 15-21
YEREMIYA 39-43
Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
• “Yehova Adzaweruza Aliyense Malinga ndi Ntchito Zake”: (10 min.)
Yer. 39:4-7—Zedekiya anakumana ndi mavuto chifukwa chosamvera Yehova (it-2-E 1228 ¶4)
Yer. 39:15-18—Yehova anayamikira Ebedi-meleki chifukwa chomukhulupirira (w12 5/1 31 ¶5)
Yer. 40:1-6—Yehova anasamalira Yeremiya yemwe anali mtumiki wake wokhulupirika (it-2-E 482)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yer. 42:1-3; 43:2, 4—Kodi tikuphunzira chiyani kuchokera pa zimene Yohanani analakwitsa? (w03 5/1 10 ¶10)
Yer. 43:6, 7—Kodi zochitika zimene zafotokozedwa m’mavesiwa zili ndi ubwino wotani? (it-1-E 463 ¶4)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 40:11–41:3
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yes. 46:10—Kuphunzitsa Choonadi. Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 12:7-9, 12—Kuphunzitsa Choonadi. Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 153 ¶19-20—Muitanireni munthuyo kumisonkhano.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Sangaiwale Chikondi Chanu” (Sal. 71:18): (15 min.) Nkhani yokambirana. Poyamba, onetsani vidiyo yakuti Yehova Sangaiwale Chikondi Chanu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia Mawu Omaliza ¶1-13
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero