Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsamba 8
  • September 27–October 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 27–October 3
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 September tsamba 8

September 27–October 3

YOSWA 6-7

  • Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musamaone Zinthu Zopanda Pake”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yos 6:20​—Kodi pali umboni wotani wosonyeza kuti mzinda wakale wa Yeriko unagonjetsedwa m’kanthawi kochepa? (w15 11/15 13 ¶2-3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 6:1-14 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (th phunziro 9)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 mfundo 3 (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 121

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.

  • Kusamvera Mwadala N’koopsa: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani mbali ina ya vidiyo yakuti ‘Palibe Ngakhale Mawu Amodzi Omwe Sanakwaniritsidwe.’ Ndipo kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi Yehova anapereka lamulo lomveka bwino liti lokhudza mzinda wa Yeriko? Kodi Akani ndi anthu a m’banja lake anachita chiyani, nanga n’chifukwa chiyani? Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhani imeneyi? Limbikitsani onse kuti akaonere vidiyo yonse kunyumba kwawo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 5 ndime 11-15, mawu akumapeto 18

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena