JUNE 2-8
MIYAMBO 16
Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Mafunso Atatu Othandiza Kusankha Zinthu Mwanzeru
(10 min.)
Kodi ndimakhulupirira kuti malangizo a Yehova akhozadi kundithandiza? (Miy 16:3, 20; w14 1/15 19-20 ¶11-12)
Kodi zomwe ndasankhazi zisangalatsa Yehova? (Miy 16:7)
Kodi ndatengeka maganizo chifukwa cha zomwe ena akulankhula kapena kuchita? (Miy 16:25; w13 9/15 17 ¶1-3)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi mafunso amenewa angandithandize bwanji kusankha zinthu mwanzeru pa nkhani ya zovala ndi kudzikongoletsa?’
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Miy 16:1-20 (th phunziro 12)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Musonyezeni mmene webusaiti ya jw.org ingamuthandizire. (lmd phunziro 2 mfundo 5)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Pemphani munthu amene anakanapo kuphunzira Baibulo m’mbuyomu kuti muziphunzira naye. (lmd phunziro 9 mfundo 5)
6. Nkhani
(5 min.) ijwbv nkhani na. 40—Mutu: Kodi Lemba la Miyambo 16:3 Limatanthauza Chiyani? (th phunziro 8)
Nyimbo Na. 32
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 27 ¶10-18