DECEMBER 1-7
YESAYA 3-5
Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Yehova Ankayembekezera Kuti Anthu Ake Azimumvera
(10 min.)
Yehova anadzala “munda wa mpesa” ndipo ankayembekezera zabwino (Yes 5:1, 2, 7; ip-1 73-74 ¶3-5; 76 ¶8-9)
“Munda wa mpesa” wa Yehova unabereka mphesa zam’tchire zokha (Yes 5:4; w06 6/15 18 ¶1)
Yehova analonjeza kuti munda wa mpesawo adzangousiya kuti ukhale wosalimidwa (Yes 5:5, 6; w06 6/15 18 ¶2)
DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi nkhani imeneyi ikundithandiza bwanji kuti ndizipewa kukhumudwitsa Yehova?’
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yes 5:8, 9—Kodi Aisiraeli ankachita chiyani chomwe chinkakhumudwitsa Yehova? (ip-1 80 ¶18-19)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yes 5:1-12 (th phunziro 5)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Gwiritsani ntchito vidiyo yapagawo lakuti Zinthu Zophunzitsira pa JW Library. (lmd phunziro 1 mfundo 5)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Muuzeni za JW Library, ndipo muthandizeni kuiika mu foni yake. (lmd phunziro 9 mfundo 5)
6. Kuphunzitsa Anthu
(5 min.) Limbikitsani wophunzira wanu amene akutsutsidwa ndi anthu a m’banja lake. (lmd phunziro 12 mfundo 4)
Nyimbo Na. 65
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 40-41