Lamlungu
“PITIRIZANI KUCHITA ZINTHU ZIMENE ZINGACHITITSE MULUNGU KUKUKONDANI”—YUDA 21
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muzikumbukira Zimene Chikondi Chimachita Komanso Zimene Sichichita
N’choleza Mtima Ndiponso N’chokoma Mtima (1 Akorinto 13:4)
Sichichita Nsanje, Sichidzitama (1 Akorinto 13:4)
Sichidzikuza, Sichichita Zosayenera (1 Akorinto 13:4, 5)
Sichisamala Zofuna Zake Zokha, Sichikwiya (1 Akorinto 13:5)
Sichisunga Zifukwa, Sichikondwera ndi Zosalungama (1 Akorinto 13:5, 6)
Chimakondwera ndi Choonadi, Chimakwirira Zinthu Zonse (1 Akorinto 13:6, 7)
Chimakhulupirira Zinthu Zonse, Chimayembekezera Zinthu Zonse (1 Akorinto 13: 7)
Chimapirira Zinthu Zonse, Chikondi Sichitha (1 Akorinto 13:7, 8)
11:10 Nyimbo Na. 150 ndi Zilengezo
11:20 NKHANI YA ONSE: Kodi Mungapeze Kuti Chikondi Chenicheni M’dziko la Anthu Opanda Chikondili? (Yohane 13:34, 35)
11:50 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
12:20 Nyimbo Na. 1 ndi Kupuma
MASANA
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 124
1:50 VIDIYO: Nkhani ya Yosiya Imatiphunzitsa Kukonda Yehova Komanso Kudana ndi Zoipa—Mbali Yachiwiri (2 Mafumu 22:3-20; 23:1-25; 2 Mbiri 34:3-33; 35:1-19)
2:20 Nyimbo, “Ndithandizeni Ndikhale Wolimba Mtima” Komanso Zilengezo
2:30 Muzichita Chidwi Ndi Ntchito za Yehova Zosonyeza Chikondi Chokhulupirika (Salimo 107:43; Aefeso 5:1, 2)
3:30 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza