Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 8/05 tsamba 6
  • Kubwereza Zophunziridwa pa Tsiku la Msonkhano Wapadera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kubwereza Zophunziridwa pa Tsiku la Msonkhano Wapadera
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
  • Nkhani Yofanana
  • Pulogalamu Yatsopano ya Tsiku la Msonkhano Wapadera
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
  • Kubwereza Zophunziridwa pa Msonkhano Wadera
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2006
  • Khalani ndi Diso la Kumodzi
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2004
  • Kodi Diso Lanu Limalunjika Pachinthu Chimodzi?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
Onani Zambiri
Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
km 8/05 tsamba 6

Kubwereza Zophunziridwa pa Tsiku la Msonkhano Wapadera

Nkhani iyi mudzaigwiritse ntchito pa pulogalamu ya Msonkhano wa Utumiki pamene tsiku la msonkhano wapadera wa chaka cha utumiki cha 2006 umene mpingo wanu udzapiteko wayandikira ndiponso mutangobwera kuchokera ku msonkhanowo. Woyang’anira wotsogolera adzakonza mmene mungachitire zimenezi mogwirizana ndi mmene unafotokozera Utumiki Wathu wa Ufumu wa August 2004, tsamba 4. Pobwerezapo, onetsetsani kuti mwafunsa mafunso onse, ndipo cholinga chachikulu chikhale kuona mmene tingagwiritsire ntchito mfundo zimene zinafotokozedwa ku msonkhanowo.

CHIGAWO CHA M’MAWA

1. Kodi kukhala ndi diso la kumodzi kumatanthauzanji, ndipo n’chifukwa chiyani kuchita zimenezi kuli kovuta masiku ano? (“N’chifukwa Chiyani Muyenera Kukhalabe ndi Diso la Kumodzi?”)

2. Kodi timapindula bwanji tikakhala ndi diso la kumodzi? (“Madalitso Amene Mungapeze Pokhalabe ndi Diso la Kumodzi”)

3. Kodi zinthu zimene timachita nthawi zonse zomwe zimaoneka kuti pazokha si zoipa zingakhale zoopsa bwanji? (“Kukhalabe ndi Diso la Kumodzi M’dziko Loipa”)

CHIGAWO CHA MASANA

4. Kodi makolo ndiponso anthu ena, angalimbikitse bwanji achinyamata kukhala ndi zolinga zauzimu? (“Makolo Amene Amaponya Mivi Yawo Molunjika” ndi “Achinyamata Okhala ndi Zolinga Zauzimu”)

5. Kodi tingayende bwanji limodzi ndi gulu la Yehova (a) aliyense payekha? (b) monga banja? (c) monga mpingo? (“Ikani Maso Anu pa Kuyenderabe Limodzi ndi Gulu la Yehova”)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena