Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 2
  • “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Gulu Lamphamvu la Asilikali a Yehova
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Elisa Anaona Magaleta Oyaka Moto​—Kodi Inunso Mukuwaona?
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2003
  • “Nyamulani Mwana Wanu”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 2
Elisa akuonetsa mtumiki wake yemwe ali wodabwa gulu la mahatchi ndi magaleta ankhondo oyaka moto lomwe lazungulira gulu la nkhondo la Asiriya.

Elisa akuuza mtumiki wake kuti: “Ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi iwowo.”​—2Mf 6:16

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”

Elisa ndi mtumiki wake anazunguliridwa ndi adani (2Mf 6:13, 14; it-1 716 ¶4)

Elisa sanachite mantha ndipo analimbikitsa mtumiki wake (2Mf 6:15-17; w13 8/15 30 ¶2; onani chithunzi chapachikuto)

Yehova anapulumutsa Elisa ndi mtumiki wake modabwitsa (2Mf 6:18, 19, it-1 343 ¶1)

Yesu ndi gulu lake la nkhondo la kumwamba akuonerera pamene apolisi ndi asilikali akuyenda mumsewu. M’bale akuthandiza Akhristu anzake kuti alowe m’nyumba.

Adani athu alibe mphamvu tikawayerekezera ndi Yehova. Zikanakhala zotheka kuti tione kumwamba, n‘kuona mmene Yehova akugwiritsira ntchito angelo poteteza anthu ake, kodi mukuganiza kuti tikanaona zotani?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena