Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 10
  • Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Anachita Zimene Anthu Sankayembekezera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 10
Yesu ndi gulu lake lankhondo lakumwamba akwera mahatchi oyera kupita kukawononga adani a Mulungu padziko lapansi.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire

Yehova analola kuti Asiriya agonjetse Aisiraeli (2Mf 17:5, 6; it-2 908 ¶5)

Yehova analanga anthu ake chifukwa ankapitiriza kuchita zinthu zoipa (2Mf 17:9-12; it-1 414-415)

Yehova anachita zinthu moleza mtima ndi Aisiraeli ndipo anawachenjeza mobwerezabwereza (2Mf 17:13, 14)

Atate wathu wachikondi Yehova, amachita zinthu moleza mtima ndi anthu opanda ungwirofe. (2Pe 3:9) Komabe, kuti akwaniritse cholinga chake, posachedwapa achitapo kanthu ndipo awononga anthu onse oipa. Kodi zimenezi zingatilimbikitse bwanji kuti tizikonza zimene timalakwitsa komanso kulalikira uthenga wabwino mwamsanga?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena