Salimo 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu, ndipulumutseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa lilengeze mosangalala kuti ndinu wolungama.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:14 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 16
14 Inu Mulungu, ndipulumutseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa lilengeze mosangalala kuti ndinu wolungama.+