Salimo 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:14 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 16
14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+