Yesaya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsiku limenelo, akazi 7 adzagwira mwamuna mmodzi+ nʼkumuuza kuti: “Ife tizidya chakudya chathuNdipo tizidzipezera tokha zovala.Inuyo mungotilola kuti tizitchedwa ndi dzina lanuKuti tichotse kunyozeka kwathu.”*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Yesaya 1, tsa. 60
4 Tsiku limenelo, akazi 7 adzagwira mwamuna mmodzi+ nʼkumuuza kuti: “Ife tizidya chakudya chathuNdipo tizidzipezera tokha zovala.Inuyo mungotilola kuti tizitchedwa ndi dzina lanuKuti tichotse kunyozeka kwathu.”*+