Yesaya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’tsiku limenelo, akazi 7 adzagwira mwamuna mmodzi+ n’kumuuza kuti: “Ife tizidya chakudya chathu ndipo tizivala zovala zathu. Inuyo mungotilola kuti tizitchedwa ndi dzina lanu kuti tichotse chitonzo chathu.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Yesaya 1, tsa. 60
4 M’tsiku limenelo, akazi 7 adzagwira mwamuna mmodzi+ n’kumuuza kuti: “Ife tizidya chakudya chathu ndipo tizivala zovala zathu. Inuyo mungotilola kuti tizitchedwa ndi dzina lanu kuti tichotse chitonzo chathu.”+