Yesaya 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tcherani khutu lanu ndipo mubwere kwa ine.+ Mverani ndipo mudzapitiriza kukhala ndi moyo,Ndithu ine ndidzachita nanu pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale+Lokhudza chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:3 Yesaya 2, ptsa. 236-238 Nsanja ya Olonda,3/1/1986, ptsa. 29-30
3 Tcherani khutu lanu ndipo mubwere kwa ine.+ Mverani ndipo mudzapitiriza kukhala ndi moyo,Ndithu ine ndidzachita nanu pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale+Lokhudza chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.+