Machitidwe 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu ameneyu, amene anaperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu+ ndi kudziwiratu kwake zamʼtsogolo, munachititsa kuti aphedwe pokhomeredwa pamtengo ndi anthu osamvera malamulo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:23 Galamukani!,8/8/1993, ptsa. 12-13 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 12
23 Munthu ameneyu, amene anaperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu+ ndi kudziwiratu kwake zamʼtsogolo, munachititsa kuti aphedwe pokhomeredwa pamtengo ndi anthu osamvera malamulo.+