2 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Panopa andisungira chisoti chachifumu cha olungama.+ Ambuye, woweruza wachilungamo,+ adzandipatsa mphotoyi pa tsikulo.+ Sikuti adzapatsa ine ndekha, koma adzapatsanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere. 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 276-277
8 Panopa andisungira chisoti chachifumu cha olungama.+ Ambuye, woweruza wachilungamo,+ adzandipatsa mphotoyi pa tsikulo.+ Sikuti adzapatsa ine ndekha, koma adzapatsanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere.