Yeremiya 50:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Anthu inu munali kusangalala,+ ndipo munali kukondwera pamene munali kulanda cholowa changa.+ Munali kudumphadumpha pamsipu ngati ng’ombe yaikazi yosaberekapo+ ndipo munali kulira ngati mahatchi amphongo.+
11 “Anthu inu munali kusangalala,+ ndipo munali kukondwera pamene munali kulanda cholowa changa.+ Munali kudumphadumpha pamsipu ngati ng’ombe yaikazi yosaberekapo+ ndipo munali kulira ngati mahatchi amphongo.+