Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w23 May tsamba 32
  • Mfundo Zothandiza Pophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mfundo Zothandiza Pophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Malifalensi a pa LAIBULALE YA PA INTANETI
  • Buku Lothandiza Kufufuza Nkhani
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Gwiritsani Ntchito Webusaiti Yathu Yovomerezeka Pophunzira Panokha Komanso Pophunzira ndi Banja Lanu
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
  • Mfundo Zothandiza Pophunzira
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Kodi Ndi Bwino Kucheza pa Intaneti?
    Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
w23 May tsamba 32

Mfundo Zothandiza Pophunzira

Malifalensi a pa LAIBULALE YA PA INTANETI

Malifalensi athu angakuthandizeni kuphunzira zambiri pa nkhani zosiyanasiyana. Malifalensiwa akuphatikizapo Matanthauzo a Mawu Ena, Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani, Insight on the Scriptures ndi Watch Tower Publications Index.

Mbali yofufuzira yomwe ili palaibulaleyi ingakuthandizeni kuti muzigwiritsa ntchito malifalensiwa. Mukamalemba mukabokosi kofufuzira, zina zomwe mukufuna zimayamba kuoneka pansi pakabokosiko. Mawu akuti “Mawu” amaonekera pambali pa liwu lililonse lomwe likupezeka m’malifalensiwo.

Tayesani izi: Pakabokosi kofufuzira (A) yambani kulemba mawu akuti “Yehova.” Pa (B) sankhani mawu akuti “Yehova” omwe ali ndi mawu akuti “Mawu” pambali pake. Mukatero muona zotsatira za m’malifalensi osiyanasiyana.

Mbali yofufuzira ya pa “LAIBULALE YA PA INTANETI.” Chizindikiro cha A, chikusonyeza mawu omwe alembedwa pa kagawo kofufuzira. Pa B, pakusonyeza mawu akuti “Mawu” omwe ali pambali pa mawu ena omwe apezeka.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena