1 ATESALONIKA
Za m’Bukuli
1
2
Utumiki wa Paulo ku Tesalonika (1-12)
Atesalonika analandila mau a Mulungu (13-16)
Paulo anali kulakalaka kuona Atesalonika (17-20)
3
Mwankhawa, Paulo ali ku Atene ndipo ayembekezela lipoti la ku Tesalonika (1-5)
Timoteyo abweletsa lipoti lolimbikitsa (6-10)
Apemphelela Atesalonika (11-13)
4
Awacenjeza kuti azipewa ciwelewele (1-8)
Mupitilize kukondana kwambili (9-12)
Amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambilila kuuka (13-18)
5