Mau Oyamba
KODI INU MUONA BWANJI?
Kodi mukhulupilila kuti mau awa adzakwanilitsidwa?
“Mulungu . . . adzapukuta misozi yonse m’maso mwao, ndipo imfa sidzakhalaponso.”—Chivumbulutso 21: 3, 4.
Nsanja ya Mlonda iyi ifotokoza mmene Mulungu adzakwanilitsila lonjezo limeneli ndi mmene mudzapindulila.