LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 4/13 tsa. 7
  • Ndandanda ya Mlungu wa April 29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa April 29
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Tumitu
  • MLUNGU WA APRIL 29
Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
km 4/13 tsa. 7

Ndandanda ya Mlungu wa April 29

MLUNGU WA APRIL 29

Nyimbo 50 ndi Pemphelo

□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:

bt mutu 22 ndime 7-14 ndi mabokosi patsamba 174 ndi 177 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibo: Luka 22-24 (Mph. 10)

Kubweleza za m’Sukulu Yaulaliki (Mph. 20)

□Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 56

Mph. 10: Kuyambitsa Phunzilo pa Ciŵelu Coyamba. Mwa kugwilitsila nchito maulaliki acitsanzo amene ali patsamba 8, onetsani mmene tingayambitsile phunzilo pa Ciŵelu coyamba mu May. Limbikitsani onse kutengamo mbali. Kambilanani nkhani yakuti “Kodi Nthawi Zonse Mumayang’anapo pa Boodi ya Zilengezo?”

Mph. 10: Uthenga Umene Tiyenela Kulengeza—“Uthenga Wabwino Uwu wa Ufumu.” Nkhani yogwila mtima yocokela m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 279 mpaka tsamba 281.

Mph. 10: Tiphunzilapo Ciani? Ŵelengani Mateyu 16:21-23; ndi Luka 9:22-26 ndipo kambilanani mmene malembawa angatithandizile mu utumiki.

Nyimbo 117 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani