LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 4
  • Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Ezara Aphunzitsa Cilamulo ca Mulungu
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Mungakhalebe na Cidalilo mu Nthawi Zovuta
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Yehova Amafuna Anthu Omutumikila Mocita Kufuna Okha
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke

Ezara analola Mawu a Mulungu kutsogolela mtima wake na khalidwe lake (Ezara 7:10; w00 10/1 14 ¶8)

Kudzela mwa Ezara, anthu ena anaona nzelu za Mulungu (Ezara 7:25; si 75 ¶5)

Cifukwa cakuti Ezara anadzicepetsa pamaso pa Mulungu, sanakayikile kuti Yehova adzamutsogolela na kum’teteza (Ezara 8:21-23; it-1 1158 ¶4)

Bwana akuyamikila m’bale amene ni wanchito wake pa sitolo yokonzela mamotoka.

Popeza kuti Ezara anaonetsa nzelu yaumulungu, mfumu inamupatsa maudindo aakulu. Mofanana na Ezara, tingabweletse citamando pa Yehova mwa khalidwe lathu

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi anthu amene si Mboni amanilemekeza cifukwa cakuti nimatsatila mfundo za Mulungu za makhalidwe abwino?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani