CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 48-50
Acikulile Ali na Zambili Zotiphunzitsa
48:21, 22; 49:1; 50:24, 25
Acikulile amalimbitsa cikhulupililo cathu mwa Yehova na malonjezo ake, akamatiuza “nchito . . . zodabwitsa” zimene aona Yehova akucita m’masiku otsiliza ano. (Sal. 71:17, 18) Ngati muli na acikulile mu mpingo wanu, afunseni za
mmene Yehova anawathandizila kugonjetsa zopinga pom’tumikila
kuwonjezeleka kwa ciŵelengelo ca olengeza Ufumu kumene aona
cimwemwe cimene amakhala naco cifukwa ca kamvedwe katsopano ka coonadi ca m’Baibo
masinthidwe amene aona m’gulu la Yehova