LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 6/14 tsa. 8
  • Maulaliki Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki Acitsanzo
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Nkhani Zofanana
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
Onaninso Zina
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 6/14 tsa. 8

Maulaliki Acitsanzo

Kuyambitsa Maphunzilo a Baibulo pa Ciŵelu Coyamba mu July

“Kodi muganiza kuti mapemphelo athu Mulungu amawaona bwanji? Kodi amawaona kukhala ofunika kapena amangowavomeleza cabe?” Yembekezani ayankhe. Kenako muonetseni kucikuto comaliza ca Nsanja ya Mlonda ya July 1, ndiyeno ŵelengelani pamodzi ndime imene ili munsi mwa funso loyamba ndi lemba limodzi limene lili pamenepo. Mugaŵileni magazini ndi kupangana zakuti mukabwelenso kudzakambilana funso lotsatila.

Nsanja ya Mlonda July 1

“Popeza kuti Mulungu ndi wamphamvuyonse, kodi muganiza kuti ndiye amacititsa zinthu zoipa zonse zimene zimacitika padziko lapansi? [Yembekezani ayankhe. Ndiyeno ŵelengani Yakobo 1:13.] Magazini iyi ifotokoza cifukwa cake zinthu zoipa zimacitika, ndi zimene Mulungu adzacita kuti athetse zinthu zoipa ndi kuvutika.”

Galamukani! July

“Nthawi iliyonse, pafupifupi munthu aliyense amakumana ndi zovuta zosiyanasiyana monga ngozi zacilengedwe, matenda oika moyo paciswe kapena imfa ya wokondedwa wathu. Zinthu zimenezi zikacitika, kodi muganiza kuti m’pofunika kukhala ndi maganizo oyenela? [Yembekezani ayankhe.] Ambili apeza kuti Baibulo lawathandiza kwambili polimbana ndi zovuta. [Ŵelengani Aroma 15:4.] Magazini iyi ikufotokoza mmene Baibulo lingatithandizile tikakumana ndi zovuta.”

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani