LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 9/14 tsa. 4
  • Maulaliki Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki Acitsanzo
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Nkhani Zofanana
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
Onaninso Zina
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 9/14 tsa. 4

Maulaliki Acitsanzo

Kuyambitsa Maphunzilo a Baibulo pa Ciŵelu Coyamba mu October

“Popeza kuti masiku ano pali zipembedzo zambili kuposa kale, tikucezelani mwacidule kuti tikambilane funso ili. [Onetsani mwininyumba funso loyamba limene lili kumbuyo kwa Nsanja ya Mlonda ya September-October.] Kodi inu muona bwanji?” Yembekezani ayankhe. Kenako, kambilanani nkhani imene ili munsi mwa funsolo, ndipo ŵelengani naye lemba ngakhale limodzi. Kenako mpatseni magazini ndi kupangana naye kuti mudzakambilane funso lotsatila pa ulendo wotsatila.”

Nsanja ya Mlonda September–October

“Mukanafuna kuti Mulungu apeleke umboni wosonyeza kuti amacita nanu cidwi, kodi mungafune kuti acite ciani?” [Yembekezani ayankhe.] Onani zimene Mau ake amakamba pofotokoza mmene Mulungu amatikondela tonsefe. [Ŵelengani Mateyu 18:14.] Magazini iyi ifotokoza njila zambili za mmene Mulungu amasonyezela kuti amatikonda.”

Galamukani! October

“Tikucezela anthu mwacidule kuti tiwathandize kupeza yankho la funso ili. [Aonetseni cikuto ca Galamukani!] Kodi muganiza kuti munthu amafunika kukhala ndi cuma kuti akhaledi wosangalala? [Yembekezani ayankhe.] Baibulo limafotokoza mmene tiyenela kuonela cuma. [Ŵelengani Luka 12:15.] Malinga ndi zimene Baibulo limanena, munthu aliyense angakhale ndi umoyo wosangalala. Magaziniyi ikukamba zambili pankhaniyi.”

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani