Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Nehemiya 10:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Komanso tizibweretsa ufa woyambirira wamisere,+ zopereka zathu, zipatso za mtengo uliwonse,+ vinyo watsopano ndi mafuta+ kwa ansembe mʼzipinda zosungira katundu* mʼnyumba ya Mulungu wathu.+ Tifunikanso kubweretsa chakhumi kwa Alevi pa zinthu zochokera mʼdziko lathu+ chifukwa Aleviwo ndi amene amatolera chakhumi kuchokera mʼmizinda yathu yonse ya zaulimi.

  • Nehemiya 12:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Mʼmasiku a Zerubabele+ komanso a Nehemiya, Aisiraeli onse ankapereka magawo a chakudya kwa oimba+ ndi alonda apageti+ mogwirizana ndi zimene ankafunikira tsiku lililonse. Ankaikanso padera gawo lina la Alevi+ ndipo Aleviwo ankaikanso padera gawo la mbadwa za Aroni.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani