Genesis 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pofika tsiku la 7, Mulungu anali atamaliza ntchito yake imene anali kuchita. Pa tsiku la 7 limenelo, iye anayamba kupuma pa ntchito yake yonse imene anali kuchita.+ Yesaya 40:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi iwe sukudziwa kapena kodi sunamve?+ Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, ndiye Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angadziwe zimene iyeyo amazimvetsa.+ Aheberi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti penapake, ponena za tsiku la 7, anati: “Ndipo Mulungu anapuma pa ntchito zake zonse pa tsiku la 7.”+
2 Pofika tsiku la 7, Mulungu anali atamaliza ntchito yake imene anali kuchita. Pa tsiku la 7 limenelo, iye anayamba kupuma pa ntchito yake yonse imene anali kuchita.+
28 Kodi iwe sukudziwa kapena kodi sunamve?+ Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, ndiye Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angadziwe zimene iyeyo amazimvetsa.+
4 Pakuti penapake, ponena za tsiku la 7, anati: “Ndipo Mulungu anapuma pa ntchito zake zonse pa tsiku la 7.”+