Ekisodo 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako utenge zovala+ zija ndi kuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi.* Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa. Efodiyo um’mange bwino ndi lamba wake.+ Ekisodo 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 zovala zosokedwa bwino ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe,+ Ekisodo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Apangenso zovala+ zosokedwa bwino zoti azivala potumikira m’malo opatulika, zovala zopatulika+ za Aroni wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.’”
5 Kenako utenge zovala+ zija ndi kuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi.* Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa. Efodiyo um’mange bwino ndi lamba wake.+
10 zovala zosokedwa bwino ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe,+
19 Apangenso zovala+ zosokedwa bwino zoti azivala potumikira m’malo opatulika, zovala zopatulika+ za Aroni wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.’”