Ekisodo 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Farao anati: “Ineyo ndikulolani kupita,+ ndipo mukaperekadi nsembe kwa Yehova Mulungu wanu m’chipululu,+ koma musapite kutali kwambiri. Ndichonderereni kwa Mulungu wanu.”+ Ekisodo 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 M’chonderereni Yehova kuti aletse mabingu ndi matalala ake.+ Pamenepo ndikulolani kupita, ndipo simukhalanso kuno.”
28 Ndiyeno Farao anati: “Ineyo ndikulolani kupita,+ ndipo mukaperekadi nsembe kwa Yehova Mulungu wanu m’chipululu,+ koma musapite kutali kwambiri. Ndichonderereni kwa Mulungu wanu.”+
28 M’chonderereni Yehova kuti aletse mabingu ndi matalala ake.+ Pamenepo ndikulolani kupita, ndipo simukhalanso kuno.”