Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Pamenepo Aisiraeli ananyamula ufa wokanda wa mkate wopanda chofufumitsa. Anaunyamulira m’zokandiramo ufa pamapewa awo atazikulunga m’nsalu zawo.

  • Ekisodo 23:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Muzitumikira Yehova Mulungu wanu,+ ndipo adzakudalitsani ndi chakudya ndi madzi.+ Ndipo ndidzachotsa matenda pakati panu.+

  • Rute 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo iye limodzi ndi apongozi ake anakonzekera ulendo wochoka kudziko la Mowabu, chifukwa ali kumeneko anamva kuti Yehova wakumbukira anthu ake+ powapatsa chakudya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena