Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pamenepo Mose anatenga magaziwo ndi kuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndiwo magazi okhazikitsira pangano+ limene Yehova wapangana nanu mwa mawu onsewa.”

  • Yohane 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.

  • Machitidwe 15:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma okhulupirira ena, amene kale anali m’gulu lampatuko la Afarisi anaimirira m’mipando yawo n’kunena kuti: “M’pofunika kuwadula+ ndi kuwalamula kuti azisunga chilamulo cha Mose.”+

  • 1 Akorinto 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pakuti m’chilamulo cha Mose muli mawu akuti: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Kodi ndi ng’ombe zimene Mulungu akusamalira?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena