1 Mafumu 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 “Adalitsike Yehova+ amene wapatsa anthu ake Aisiraeli malo ampumulo, monga mwa zonse zimene analonjeza.+ Palibe mawu ndi amodzi omwe+ amene sanakwaniritsidwe pa malonjezo ake onse abwino amene analonjeza kudzera mwa Mose mtumiki wake.+ 1 Mbiri 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Davide anachita zimenezi popeza anati: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wapereka mpumulo kwa anthu ake,+ ndipo iye adzakhala mu Yerusalemu mpaka kalekale.+ Aheberi 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ngati Yoswa+ anawalowetsa m’malo ampumulo,+ Mulungu sakananenanso pambuyo pake+ za tsiku lina.
56 “Adalitsike Yehova+ amene wapatsa anthu ake Aisiraeli malo ampumulo, monga mwa zonse zimene analonjeza.+ Palibe mawu ndi amodzi omwe+ amene sanakwaniritsidwe pa malonjezo ake onse abwino amene analonjeza kudzera mwa Mose mtumiki wake.+
25 Davide anachita zimenezi popeza anati: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wapereka mpumulo kwa anthu ake,+ ndipo iye adzakhala mu Yerusalemu mpaka kalekale.+
8 Pakuti ngati Yoswa+ anawalowetsa m’malo ampumulo,+ Mulungu sakananenanso pambuyo pake+ za tsiku lina.