Ekisodo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga ndi kukubweretsani kwa ine.+ Deuteronomo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova yekha anapitiriza kumutsogolera,+Ndipo panalibe mulungu wachilendo kuwonjezera pa iye.+ Amosi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ine ndinatulutsa anthu inu m’dziko la Iguputo+ ndi kukuyendetsani m’chipululu zaka 40+ kuti mukatenge dziko la Aamori.+
4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga ndi kukubweretsani kwa ine.+
10 Koma ine ndinatulutsa anthu inu m’dziko la Iguputo+ ndi kukuyendetsani m’chipululu zaka 40+ kuti mukatenge dziko la Aamori.+