Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Ngati pali mlendo amene akukhala pakati panu, iyenso azikonza nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova.+ Aziikonza motsatira malamulo onse a pasika, ndiponso kakonzedwe kake ka nthawi zonse.+ Pakhale malamulo ofanana kwa nonsenu, kaya mlendo kapena mbadwa.’”+

  • 2 Mafumu 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako iye pamodzi ndi gulu lake lonse anabwerera kwa munthu wa Mulungu woona+ uja. Anaima pamaso pake n’kunena kuti: “Tsopano ndadziwa ndithu kuti, padziko lonse lapansi kulibenso kwina kumene kuli Mulungu kupatula ku Isiraeli kokha.+ Ndiye landirani mphatso+ kuchokera kwa ine mtumiki wanu.”

  • 2 Mbiri 6:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Komanso mlendo amene sali mmodzi wa anthu anu Aisiraeli,+ amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina lanu lalikulu,+ ndi dzanja lanu lamphamvu+ ndi mkono wanu wotambasuka,+ ndipo iwo abwera n’kupemphera atayang’ana nyumba ino,+

  • Yesaya 56:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Alendo amene adziphatika kwa Yehova kuti am’tumikire+ ndiponso amene amakonda dzina la Yehova+ n’cholinga choti akhale atumiki ake, onse amene amasunga sabata kuti asalidetse ndiponso amene amatsatira pangano langa,+

  • Machitidwe 8:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho, ananyamuka ndi kupita. Kumeneko anakumana ndi nduna+ ya ku Itiyopiya,+ munthu waulamuliro pansi pa Kandake, mfumukazi ya Itiyopiya. Iye anali woyang’anira chuma chonse cha mfumukaziyo. Iyeyu anapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena