Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Iye adzaonetsa poyera kulungama kwako kuti kuunike ngati kuwala,+

      Adzaonetsa poyera chilungamo chako kuti chiwale ngati usana.+

  • Danieli 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Poona zimenezi, nduna zapamwamba ndi masatarapi aja nthawi zonse anali kufunafuna chomunamizira Danieli pa kayendetsedwe kake ka zinthu mu ufumuwo.+ Koma iwo sanapeze chifukwa chilichonse chomunamizira kapena chinthu chilichonse chachinyengo chimene anachita, pakuti iye anali wokhulupirika. Iwo anapeza kuti Danieli sanali kunyalanyaza kanthu kapena kuchita zachinyengo zilizonse.+

  • 1 Timoteyo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena