Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+

  • Oweruza 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno mu Betelehemu+ wa ku Yuda munali mnyamata wina, wa m’banja la Yuda, ndipo anali Mlevi.+ Iye anakhala kumeneko kwa kanthawi.

  • Rute 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndipo anapitiriza ulendo wawo mpaka anafika ku Betelehemu.+ Atangofika ku Betelehemu, anthu mumzinda wonsewo anayamba kulankhula za iwo.+ Akazi anali kufunsa kuti: “Kodi si Naomi+ uyu?”

  • Rute 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo anthu onse ndi akulu amene anali pachipata anayankha kuti: “Ndife mboni! Yehova adalitse mkazi amene akulowa m’nyumba mwako kuti akhale ngati Rakele+ ndi Leya,+ akazi amene anabereka ana a nyumba ya Isiraeli.+ Uonetse kulemekezeka kwako mu Efurata+ ndi kudzipangira dzina m’Betelehemu.+

  • 1 Samueli 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Patapita nthawi, Yehova anauza Samueli kuti: “Kodi ulirira Sauli+ mpaka liti, pamene ine ndamukana kuti alamulire monga mfumu ya Isiraeli?+ Thira mafuta m’nyanga yako+ ndipo unyamuke. Ndikutumiza kwa Jese+ wa ku Betelehemu, chifukwa ndapeza munthu pakati pa ana ake aamuna woti akhale mfumu yanga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena