Ekisodo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku lachitatu kutacha, kunayamba kuchita mabingu ndi mphezi.+ Mtambo wakuda+ unakuta phiri, ndipo kunamveka kulira kwamphamvu kwambiri kwa lipenga la nyanga ya nkhosa,+ moti anthu onse mumsasawo anayamba kunjenjemera.+ 1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+
16 Pa tsiku lachitatu kutacha, kunayamba kuchita mabingu ndi mphezi.+ Mtambo wakuda+ unakuta phiri, ndipo kunamveka kulira kwamphamvu kwambiri kwa lipenga la nyanga ya nkhosa,+ moti anthu onse mumsasawo anayamba kunjenjemera.+
10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+