1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Tsanzirani, tsa. 57 Nsanja ya Olonda,7/1/2010, tsa. 173/15/2005, tsa. 21
10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+