-
1 Samueli 29:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho Akisi+ anaitana Davide ndi kumuuza kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ iweyo ndiwe wowongoka mtima, ndipo ndasangalala+ kuti wabwera nane+ kunkhondo, pakuti sindinapeze choipa chilichonse mwa iwe kuyambira tsiku limene unabwera kwa ine kufikira lero.+ Koma olamulira ogwirizana+ sakukuona bwino.
-