Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anamanganso mizinda ya Betelehemu,+ Etami,+ Tekowa,+

  • 2 Mbiri 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anthuwo ananyamuka m’mawa kwambiri n’kupita kuchipululu+ cha Tekowa.+ Ali m’njira, Yehosafati anaimirira n’kunena kuti: “Tamverani inu Ayuda ndi anthu okhala mu Yerusalemu!+ Khulupirirani+ Yehova Mulungu wanu kuti mukhalitse. Khulupirirani aneneri+ ake kuti zinthu zikuyendereni bwino.”

  • Nehemiya 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Atekowa+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Zadoki analekezera. Koma anthu otchuka pakati pa Atekowa+ sanagonjere ambuye awo ndi kuwatumikira.

  • Amosi 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Awa ndi mawu a Amosi amene anali mmodzi mwa anthu oweta nkhosa ku Tekowa.+ Anauzidwa mawu amenewa m’masomphenya okhudza Isiraeli,+ m’masiku a Uziya+ mfumu ya Yuda ndi m’masiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi,+ mfumu ya Isiraeli, zaka ziwiri chivomezi chisanachitike.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena