Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu,+ kumwambamwamba ndi zonse zili kumeneko, dziko lapansi+ ndi zonse zili mmenemo ndi zake zonsezo.

  • 2 Mbiri 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo ndani angakhale ndi mphamvu zomangira Mulunguyo nyumba?+ Pakuti kumwamba, ngakhale kumwambamwamba, ndi kosakwanira kuti akhaleko.+ Ndiye ine ndine ndani+ kuti ndimumangire nyumba, kupatulapo yofukiziramo nsembe yautsi pamaso pake?+

  • Nehemiya 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Inu ndinu Yehova, inu nokha.+ Ndinu amene munapanga kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba ndi makamu ake onse.+ Ndinu amene munapanga dziko lapansi+ ndi zonse zili momwemo+ komanso nyanja+ ndi zonse zili momwemo.+ Ndinu amene mukusunga zinthu zonse kuti zikhale ndi moyo. Ndipo makamu+ akumwamba amakugwadirani.

  • 2 Akorinto 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndikudziwa munthu wina wogwirizana ndi Khristu. Zaka 14 zapitazo, munthu ameneyu anakwatulidwira kumwamba kwachitatu. Kaya zimenezo zinachitika ali m’thupi kapena ali kunja kwa thupi sindikudziwa. Akudziwa ndi Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena