1 Mbiri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Heburoni anali Yeriya amene anali mtsogoleri wawo, wachiwiri wake anali Amariya, wachitatu anali Yahazieli, ndipo wachinayi anali Yekameamu.+ 1 Mbiri 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kumbali ya Aheburoni kunalinso Yereya+ mtsogoleri wa Aheburoniwo malinga ndi mibadwo ya makolo awo. M’chaka cha 40+ cha ufumu wa Davide, iwo anafunafuna anthu ndipo anapeza amuna amphamvu ndi olimba mtima pakati pawo ku Yazeri+ ku Giliyadi.+
19 Ana a Heburoni anali Yeriya amene anali mtsogoleri wawo, wachiwiri wake anali Amariya, wachitatu anali Yahazieli, ndipo wachinayi anali Yekameamu.+
31 Kumbali ya Aheburoni kunalinso Yereya+ mtsogoleri wa Aheburoniwo malinga ndi mibadwo ya makolo awo. M’chaka cha 40+ cha ufumu wa Davide, iwo anafunafuna anthu ndipo anapeza amuna amphamvu ndi olimba mtima pakati pawo ku Yazeri+ ku Giliyadi.+